"Si Lero" Tekstovi
"Si Lero" ima stihove na engleski jeziku.
"Si Lero" značenje dolazi iz engleski jezika i trenutno nije pretvoreno u engleski prijevod.
Lyrics:
INTRO
Wazizur!!
HOOK
Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Silero!!
VERSE 1
Uluruwu ndiye sukuchoka Cancer’yi ngati ndingofa mwina ndizachila koma Si lero!!
Ndaona zinthu ngati Doctor m’manjamu anthu kumangofa Ndufuna ntapuma koma Si lero!!
I know lero sizingatheke pa wheelchair’Pa one day ndizachoka inde ngakhale Si lero!!
Masten anga kuli Chete munapita ngati Bodza Nzakuonaninso ngakhale!!
HOOK
Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Silero!!
VERSE 2
Mufunse Driemo
Made it outta Ntchisi ena nkumati si iyeyo
Nawenso uzaiphula Aise ngakhale si lero
Nzothekanso kufa usanaiphulire ndiye Moyowo
Ma funso onse azayankhidwa ngakhale si lero
Wina akuyendera Manja fukwa alibe Miyendo
amasamala ziweto Suli wekha tiyeko
Ikanso ma earphone ndimvetsele mavutowa azatha ngakhale!
HOOK
Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Si lero! Silero!!
OUTRO
Si Lero! and I still believe
Si Lero! But not today Its not today